Salmos 64

NYA

1 Ndimvereni Mulungu pomwe ndikunena madandawulo anga;

2 Ndibiseni ku chiwembu cha anthu oyipa,

3 Iwo amanola malilime awo ngati malupanga,

4 Iwo amaponya mivi yawo ali pa malo wobisala kwa munthu wosalakwa;

5 Iwo amalimbikitsana wina ndi mnzake pa chikonzero chawo choyipa,

6 Iwo amakonzekera zosalungama ndipo amati,

7 Koma Mulungu adzawalasa ndi mivi;

8 Iye adzatembenuza milomo yawoyo kuwatsutsa

9 Anthu onse adzachita mantha;

10 Lolani wolungama akondwere mwa Yehova

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado