1 Landitseni kwa adani anga, Inu Mulungu;
2 Landitseni kwa anthu ochita zoyipa
3 Onani momwe iwo akundibisalira!
4 Ine sindinachite cholakwa, koma iwo ndi okonzeka kundithira nkhondo.
5 Inu Yehova Mulungu Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli,
6 Iwo amabweranso madzulo
7 Onani zomwe amalavula mʼkamwa mwawo;
8 Koma Inu Yehova, mumawaseka,
9 Inu mphamvu yanga, ine ndiyangʼana kwa inu;
10 Mulungu wanga wachikondi.
11 Koma musawaphe, Inu Ambuye chishango chathu,
12 Chifukwa cha machimo a pakamwa pawo
13 muwawononge mu ukali (wanu)
14 Iwo amabweranso madzulo,
15 Iwo amayendayenda kufuna chakudya
16 Koma ine ndidzayimba za mphamvu yanu,
17 Inu mphamvu yanga, ndiyimba matamando kwa inu;