1 Mundichitire chifundo Inu Mulungu, pakuti anthu akundithamangitsa kwambiri;
2 Ondinyoza akundithamangitsa tsiku lonse,
3 Ndikachita mantha
4 Mwa Mulungu, amene mawu ake ine ndimatamanda,
5 Tsiku lonse amatembenuza mawu anga;
6 Iwo amakambirana, amandibisalira,
7 Musalole konse kuti athawe;
8 Mulembe za kulira kwanga,
9 Adani anga adzabwerera mʼmbuyo
10 Mwa Mulungu amene mawu ake ndimawatamanda,
11 mwa Mulungu ine ndimadalira ndipo sindidzachita mantha.
12 Ndiyenera kuchita zomwe ndinalumbira kwa Mulungu;
13 Pakuti mwawombola moyo wanga ku imfa