Provérbios 18

NYA

1 Munthu wokonda kukhala yekha amafunafuna zomukomera yekha;

2 Chitsiru chilibe chidwi chomvetsa zinthu,

3 Kuyipa mtima kukabwera, manyozonso amabwera.

4 Mawu a munthu ali ngati madzi akuya,

5 Si kwabwino kukondera munthu woyipa pa milandu;

6 Mawu a chitsiru amautsa mkangano;

7 Pakamwa pa chitsiru ndipo pamabweretsa chiwonongeko chake,

8 Mawu a miseche ali ngati chakudya chokoma;

9 Munthu waulesi pa ntchito yake

10 Dzina la Yehova lili ngati nsanja yolimba;

11 Chuma cha anthu olemera chili ngati mzinda wake wolimba;

12 Chiwonongeko chisanafike, mtima wa munthu umakhala wonyada,

13 Ukayankha usanamvetse bwino nkhani,

14 Mtima wa munthu utha kupirira pa matenda,

15 Munthu wanzeru amawonjezera nzeru zina;

16 Mphatso ya munthu imamutsekulira njira

17 Amene amayamba kufotokoza mlandu wake amaoneka ngati wolungama ndiye

18 Kuchita maere kumathetsa mikangano;

19 Mʼbale amene wamuthandiza amakhala ngati mzinda wolimba,

20 Munthu amapeza bwino malingana ndi zoyankhula zake.

21 Mawu ako angathe kukuphetsa kapena kukukhalitsa moyo.

22 Wapeza mkazi wapeza chinthu chabwino

23 Munthu wosauka amapempha

24 Pali abwenzi amene chibwenzi chawo nʼchapamaso,

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado