1 Zolinga za mu mtima ndi za munthu,
2 Zochita zonse za munthu zimaoneka zabwino pamaso pake,
3 Pereka ntchito zako zonse mʼmanja mwa Yehova,
4 Yehova amachita zonse ndi cholinga chake,
5 Munthu aliyense wodzikuza amamunyansa Yehova.
6 Chifukwa cha chikondi chosasinthika ndi kukhulupirika, munthu amakhululukidwa machimo ake;
7 Pamene makhalidwe a munthu akondweretsa Yehova,
8 Kuli bwino kukhala ndi zinthu pangʼono zozipeza mwachilungamo,
9 Mtima wa munthu umalingalira zochita,
10 Mawu a mfumu ali ngati mawu ochokera kwa Mulungu;
11 Miyeso ndi masikelo achilungamo zimachokera kwa Yehova;
12 Kuchita zoyipa kumanyansa mafumu,
13 Mawu owona amakondweretsa mfumu.
14 Ukali wa mfumu ndi mthenga wa imfa,
15 Kuwala kwa nkhope ya mfumu kumapatsa moyo;
16 Nʼkwabwino kwambiri kupeza nzeru kupambana golide.
17 Msewu wa munthu wowongoka mtima umapewa zoyipa;
18 Kunyada kumafikitsa ku chiwonongeko,
19 Nʼkwabwino kukhala ndi mtima wodzichepetsa pakati pa anthu oponderezedwa,
20 Munthu womvera malangizo zinthu zimamuyendera bwino,
21 A mtima wanzeru amatchedwa ozindikira zinthu,
22 Kumvetsa zinthu ndi kasupe wa moyo kwa iwo amene ali nako,
23 Mtima wanzeru umathandiza munthu kuyankhula mwa nzeru,
24 Mawu okometsera ali ngati chisa cha njuchi,
25 Pali njira ina yooneka ngati yowongoka kwa munthu
26 Njala ya munthu wantchito imamuthandiza kulimbikira;
27 Munthu wopanda pake amakonzekera kuchita zoyipa
28 Munthu woyipa mtima amayambitsa mikangano,
29 Munthu wandewu amakopa mnansi wake,
30 Amene amatsinzinira maso ake amalingalira zinthu zokhota;
31 Imvi zili ngati chipewa chaufumu chaulemerero;
32 Munthu wosapsa mtima msanga amaposa munthu wankhondo,
33 Maere amaponyedwa pa mfunga,