1 Iwe mzinda wa anthu ankhondo, sonkhanitsa anthu ako ankhondo,
2 “Koma iwe Betelehemu Efurata,
3 Nʼchifukwa chake Israeli adzasiyidwa
4 Iye adzalimbika, ndipo adzaweta nkhosa zake
5 Ndipo Iye adzakhala mtendere wawo.
6 Iwo adzagonjetsa dziko la Asiriya ndi lupanga,
7 Otsalira a Yakobo adzakhala
8 Otsala a Yakobo adzakhala pakati pa mitundu ya anthu,
9 Mudzagonjetsa adani anu,
10 Yehova akuti,
11 Ndidzawononga mizinda ya mʼdziko mwanu
12 Ndidzawononga ufiti wanu
13 Ndidzawononga mafano anu osema
14 Ndidzazula mitengo ya mafano a Asera imene ili pakati panu,
15 Ndidzayilanga mwaukali ndi mokwiya