1 Yehova akuti,
2 Ndi wodala munthu amene amachita zimenezi,
3 Mlendo amene waphatikana ndi Yehova asanene kuti,
4 Popeza Yehova akuti,
5 ndidzawapatsa dzina ndi mbiri yabwino
6 Yehova akuti, “Alendo amene amadziphatika kwa Yehova,
7 amenewa Ine ndidzawafikitsa ku phiri langa lopatulika,
8 Ambuye Yehova, amene amasonkhanitsa
9 Bwerani, inu zirombo zonse zakuthengo,
10 Atsogoleri onse a Israeli ndi akhungu,
11 Ali ngati agalu amene ali ndi njala yayikulu;
12 Aliyense amafuwulira mnzake kuti, “Bwera, tiye timwe vinyo!