Isaías 55

NYA

1 “Bwerani, inu nonse amene muli ndi ludzu,

2 Chifukwa chiyani ndalama zanu mukuwonongera zinthu zimene samadya,

3 Tcherani makutu ndipo mubwere kwa Ine;

4 Taonani, ine ndamusankha kuti akhale mboni yanga kwa mitundu ya anthu,

5 Ndithu inu mudzayitanitsa mitundu ya anthu imene simuyidziwa,

6 Funafunani Yehova pamene Iye akupezeka.

7 Woyipa asiye makhalidwe ake oyipa,

8 “Pakuti maganizo anga siwofanana ndi maganizo anu,

9 “Monga momwe mlengalenga muli kutali ndi dziko lapansi,

10 Monga mvula ndi chisanu chowundana

11 Ndi mmenenso amachitira mawu ochokera mʼkamwa mwanga.

12 Inu mudzatuluka mu mzindawo mwachimwemwe

13 Mʼmalo mʼmene tsopano muli mitengo ya minga mudzamera mitengo ya payini,

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado