Isaías 31

NYA

1 Tsoka kwa amene amapita ku Igupto kukapempha chithandizo,

2 Komatu Yehovayo ndi wanzeru ndipo angathe kuwononga,

3 Aigupto ndi anthu chabe osati Mulungu;

4 Zimene Yehova akunena kwa ine ndi izi:

5 Monga mbalame zowuluka pamwamba pa zisa zake,

6 Inu Aisraeli, bwererani kwa Iye amene munamuwukira kwakukulu.

7 Pakuti tsiku limenelo nonsenu mudzataya mafano anu a siliva ndi golide amene mumapanga ndi manja anu auchimo.

8 “Aasiriya adzaphedwa ku nkhondo ndi mphamvu osati za munthu.

9 Mfumu yawo idzamwalira ndi mantha,

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado