1 Imvani mawu awa, inu ngʼombe zazikazi za ku Basani, okhala pa Phiri la Samariya,
2 Ambuye Yehova, mwa kuyera mtima kwake walumbira kuti,
3 Mudzatulukira mʼmingʼalu ya pa khoma
4 “Bwerani ku Beteli mudzachimwe;
5 Wotchani buledi wokhala ndi yisiti ngati nsembe yachiyamiko
6 “Ndine amene ndinakusendetsani milomo mʼmizinda yanu yonse,
7 “Ndinenso amene ndinamanga mvula
8 Anthu ankayenda mzinda ndi mzinda kufuna madzi,
9 “Nthawi zambiri ndinakantha mbewu zanu ndiponso minda ya mpesa,
10 “Ine ndinabweretsa miliri pakati panu
11 “Ndinawononga ena mwa inu
12 “Choncho izi ndi zimene ndidzakuchitire iwe Israeli,
13 Iye amene amawumba mapiri,