Isaías 9

NYA

1 Anthu amene anali ndi nkhawa, sadzakhalanso otaya mtima. Masiku amakedzana Mulungu ananyozetsa dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafutali, koma kutsogolo kuno dera lonse la Galileya, limene lili dziko la anthu a mitundu ina, kuyambira ku nyanja yayikulu, mʼmbali mwa Yorodani, adzalisandutsa laulemu.

2 Anthu oyenda mu mdima

3 Inu mwauchulukitsa mtundu wanu

4 Monga munachitira pogonjetsa Amidiyani,

5 Nsapato iliyonse ya munthu wankhondo,

6 Chifukwa mwana watibadwira,

7 Ulamuliro ndi mtendere wake

8 Ambuye atumiza mawu otsutsa Yakobo;

9 Anthu onse okhala mu

10 “Ngakhale njerwa zagumuka,

11 Koma Yehova wadzutsa adani kuti alimbane nawo

12 Asiriya ochokera kummawa ndi Afilisti ochokera kumadzulo ndipo

13 Koma anthu sanabwerere kwa amene anawakantha uja,

14 Choncho Yehova adzadula mutu wa Israeli pamodzi ndi mchira womwe,

15 mutuwo ndiye akuluakulu ndi olemekezeka,

16 Amene amatsogolera anthuwa ndiwo amawasocheretsa,

17 Nʼchifukwa chake Ambuye adzakondwera nawo achinyamata,

18 Ndithu kuyipa kwa anthuwo kumayaka ngati moto;

19 Dziko lidzatenthedwa ndi ukali wa Yehova Wamphamvuzonse,

20 Kudzanja lamanja adzapeza chakudya nʼkudya,

21 Manase adzadya Efereimu ndipo Efereimu adzadya Manase;

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado