Isaías 38

NYA

1 Nthawi imeneyo Mfumu Hezekiya anadwala ndipo anali pafupi kufa. Mneneri Yesaya mwana wa Amozi anapita kukamuona ndipo anati “Yehova akuti: Konza bwino nyumba yako, pakuti ukufa; suchira.”

2 Hezekiya anatembenuka nayangʼana kukhoma, napemphera kwa Yehova kuti,

3 “Inu Yehova, kumbukirani momwe ndayendera pamaso panu mokhulupirika ndi modzipereka ndipo ndakhala ndikuchita zabwino pamaso panu.” Ndipo Hezekiya analira mosweka mtima.

4 Ndipo Yehova analamula Yesaya kuti:

5 “Pita kwa Hezekiya ndipo ukamuwuze kuti, ‘Yehova, Mulungu wa kholo lake Davide akuti: Ndamva pemphero lako ndipo misozi yako ndayiona; ndidzakuwonjezera zaka 15 pa moyo wako.

6 Ndipo ndidzakupulumutsa, iwe pamodzi ndi mzindawu mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya, Ine ndidzawuteteza mzindawu.

7 “ ‘Ichi ndi chizindikiro cha Yehova kwa iwe kutsimikiza kuti Yehova adzachita zimene walonjeza:

8 Chithunzithunzi chimene dzuwa likuchititsa pa makwerero a Ahazi ndidzachibweza mʼmbuyo makwerero khumi.’ ” Ndipo chithunzithunzi chinabwerera mʼmbuyo makwerero khumi.

9 Ndakatulo ya Hezekiya mfumu ya ku Yuda imene analemba atadwala ndi kuchira:

10 Ine ndinaganiza kuti

11 Ndinaganiza kuti, “Sindidzaonanso Yehova,

12 Nyumba yanga yasasuka

13 Ndinkalira kupempha chithandizo usiku wonse mpaka mmawa;

14 Ndinkalira ngati namzeze kapena chumba,

15 Koma ine ndinganene chiyani?

16 Ambuye, masiku anga ali mʼmanja mwanu.

17 Ndithudi, ine ndinamva zowawa zotere

18 Pakuti akumanda sangathe kukutamandani,

19 Amoyo, amoyo okha ndiwo amakutamandani,

20 Yehova watipulumutsa.

21 Yesaya anati, “Anthu atenge mʼbulu wankhunyu ndipo apake pa chithupsacho ndipo Hezekiya adzachira.”

22 Hezekiya nʼkuti atafunsa kuti, “Kodi chizindikiro chako nʼchiyani chotsimikiza kuti ndidzapita ku Nyumba ya Yehova?”

Ler em outra tradução

Comparar lado a lado